A-Z Lyrics Database
Welcome! Login | Register
Lyrics   »   L   »   Langwan Piksy Lyrics   »   Maso Lyrics

Langwan Piksy - Maso Lyrics

Font:      
Align:    
  • VERSE 1
  • Ndakhalilidwa
  • Ndakankhidwa
  • Ndakanidwa
  • Ndasalidwa
  • Ndapanidwa
  • But I didn’t go down
  • Yeah ena ankati sindingazithe
  • Malo ena sinnapite
  • Zinawawa koma look at me now
  • Ey
  • You know, nthawi zina tima manga ndende tokha
  • Zabwino zochulukitsa tokha tima blocker
  • Timafuna zophweka zikavuta tima dropper
  • Kudikira ena ayambe ife tingokopa
  • Anthu ochuluka they wanna see me begging
  • Kuyamba ngati othandiza they wanna leave me hanging
  • Pankhope ngati a chifundo but I know they faking
  • Pankhope a chikondi kumbaliko nde ndisekeni
  • People take your kindness for a weakness
  • Kusiya zawo uko they mind your business
  • You know, sometimes ndi bwino kumasunga chinsinsi
  • Kukhala wekha bola mu mtima wako muli peace
  • (amen)
  • CHORUS
  • So many things I can thank god for
  • Madalitso ndaona ndi maso
  • Anali nane pompo
  • Pomwe panali khoma anayikapo khomo
  • Yeah
  • So many things I can thank God for
  • Madalitso ndawaona ndi maso
  • Zomwe ankati sizingandichitikire
  • Ndaziona ndi maso
  • VERSE 2
  • Musanandide mufunse komwe ndachoka
  • Mukanakhala ine ena a inu mukanafoka
  • I lost hope
  • It got too hard to cope
  • Everything felt so wrong
  • Man it’s been….hard for me
  • Maloto far from real
  • Lero mphamvu ndzipeza ain no stopping me
  • Ndingati ku maloto nkamaona success
  • Onse munayima nane nyengo iyi God bless
  • Whoever thought ndidzafika this far?
  • Ndinali mnyamata pano ndi Mister
  • Anthu ochuluka callin’ me star
  • Nsanje ayi mudzinditcha victor
  • Lero zinthu zimasintha when I step in
  • Mphepo ingadze molimba im not shaken
  • Ndimangoseka
  • Zikuphweka
  • Mulungu wadalitsa zonse zongotheka
  • CHORUS
  • So many things I can thank god for
  • Madalitso ndaona ndi maso
  • Anali nane pompo
  • Pomwe panali khoma anayikapo khomo
  • Yeah
  • So many things I can thank God for
  • Madalitso ndawaona ndi maso
  • Zomwe ankati sizingandichitikire
  • Ndaziona ndi maso
  • VERSE 3
  • Anthu amene andikondane zeni zeni
  • (ndawaona ndi maso)
  • Adani anga onse ali pa ntetete
  • (ndawaona ndi maso)
  • Chisomo chanu position kuchita maintain
  • (ndachiona ndi maso)
  • Chikondi ndachiona ndi maso…maso…maso
  • CHORUS
  • So many things I can thank god for
  • Madalitso ndaona ndi maso
  • Anali nane pompo
  • Pomwe panali khoma anayikapo khomo
  • Yeah
  • So many things I can thank God for
  • Madalitso ndawaona ndi maso
  • Zomwe ankati sizingandichitikire
  • Ndaziona ndi maso

  • Report error in lyric




    The Maso lyrics by Langwan Piksy is property of their respective authors, artists and labels and are strictly for non-commercial use only.
    Copyright © 2009-2026 Azlyricdb.com. All Rights Reserved | Privacy policy | Blog
    You are now viewing Langwan Piksy Maso Lyrics