Langwan Piksy - Mthunzi Lyrics
CHORUSNdikufuna mthunziwoSindufuna NkhunizoChonde musaduleMtengo wangawoNthawi zina sitikamba zofunika kukambidwaSitikankha zofunika kukankhidwaPena Sitikanda pofunika kukandidwaDziko linasintha timaopa kutayidwaMa born againSangacheze nawe unless you born againBut then againNdingasinthe bwanji ngati muku leader life ngati muli kumwamba kaleU seem so far awayYesu anadzera ochimwaMiyala yokanidwayoThese days ndiimene ikusalidwayoThink againIf you really born againNjira yanuyo tilondolereniCHORUSNdikufuna mthunziwoSindufuna NkhunizoChonde musaduleMtengo wangawoAbambo prophet akazi awo prophetessChondidabwitsa amakhala ndi confidenceIne I thought zimayendera maitanidweMesa ndimphatsoYoti ena alibePa banja panu mwayambisa yanu churchDzina lake pa Google mwachita searchTilibe mphavu zokupangirani judgeKoma ngati nku jahena chonde msatipange dragKuuza anthu amu mpingo mwanu alemeraAkhristu anu kupusa amayamba kusekeleraAmen!Mulungu achita kothekeraKusiya kulimbikira ntchito nkumangopempheraKenako amayamba nsanjeMwawasocheretsaKukhulupira ulosi wanu mwawasokonezaAwa nga satanicAwa kukhwima chabe awaNeba wachikunja walemera mtima ukuwawaCHORUSNdikufuna mthunziwoSindufuna NkhunizoChonde musaduleMtengo wangawoMutiuze za kumwambaOsati kumangotikomedwetsa nzapadziko panoPanoMuzinthu zonse, zonse zonseAmbuye akhalemoAmatero malemboUpindulanji ndi za mdziko ukutaya moyo wako?Musachulutse zokamba kuti tidzikuopaniTidzikweza Mulungu osati tidzikupopaniTidziona umulungu tikamakuonaniSing along to the songMuzinthu zonse, zonse, zonseMuzinthu zonse Ambuye akhalemoCHORUSNdikufuna mthunziwoSindufuna NkhunizoChonde musaduleMtengo wangawo